Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 39:2 - Buku Lopatulika

2 Ndinatonthola osanena mau, ndinakhala chete osalawa chokoma; ndipo chisoni changa chinabuka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndinatonthola osanena mau, ndinakhala chete osalawa chokoma; ndipo chisoni changa chinabuka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Motero ndidakhala chete osalankhula kanthu, ndidakhala duu, koma popanda phindu, chifukwa mavuto anga ankangokulirakulira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Koma pamene ndinali chete osanena ngakhale kanthu kalikonse kabwino mavuto anga anachulukirabe.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 39:2
10 Mawu Ofanana  

Mundiphunzitse, Yehova, njira ya malemba anu; ndidzaisunga kufikira kutha kwake.


Mundizindikiritse, ndipo ndidzasunga malamulo anu; ndidzawasamalira ndi mtima wanga wonse.


Muike mdindo pakamwa panga, Yehova; sungani pakhomo pa milomo yanga.


Futuka pazoipa, nuchite zabwino, funa mtendere ndi kuulondola.


Iye anatsenderezedwa koma anadzichepetsa yekha osatsegula pakamwa pake; ngati nkhosa yotsogoleredwa kukaphedwa, ndi ngati mwanawankhosa amene ali duu pamaso pa omsenga, motero sanatsegule pakamwa pake.


Musamapatsa chopatulikacho kwa agalu, ndipo musamaponya ngale zanu patsogolo pa nkhumba, kuti zingazipondereze ndi mapazi ao, ndi potembenuka zingang'ambe inu.


pakuti sitingathe ife kuleka kulankhula zimene tinaziona ndi kuzimva.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa