Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 39:13 - Buku Lopatulika

13 Ndiloleni, kuti nditsitsimuke, ndisanamuke ndi kukhala kuli zii.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndiloleni, kuti nditsitsimuke, ndisanamuke ndi kukhala kuli zii.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Musandiyang'ane mwaukali, choncho ndidzatha kusangalala, ndisanafe ndi kuzimirira.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Musandiyangʼane mwaukali, choncho ndidzatha kusangalala ndisanafe ndi kuyiwalika.”

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 39:13
12 Mawu Ofanana  

Ndipo Yakobo atate wao anati kwa iwo, Munandilanda ine ana; Yosefe palibe, Simeoni palibe, ndipo mudzachotsa Benjamini: zonse zimene zandigwera.


Ndipo Yakobo anati kwa Farao, Masiku a zaka za ulendo wanga ndi zaka zana limodzi kudza makumi atatu; masiku a zaka za moyo wanga ali owerengeka ndi oipa, sanafikire masiku a zaka za moyo wa makolo anga m'masiku a ulendo wao.


ndipo Enoki anayendabe ndi Mulungu; ndipo panalibe iye; pakuti Mulungu anamtenga.


Mukumbukire Yehova kuti ndinayendabe pamaso panu m'choonadi, ndi mtima wangwiro, ndi kuchita zokoma m'kuona kwanu. Nalira Hezekiya kulira kwakukulu.


Pakuti ife ndife alendo pamaso panu, ndi ogonera, monga makolo athu onse; masiku athu a padziko akunga mthunzi, ndipo palibe kukhalitsa.


Mukana kundichokera kufikira liti, kapena kundileka mpaka nditameza dovu?


Ine ndine mlendo padziko lapansi; musandibisire malamulo anu.


Pamenepo linagwedezeka, ndi kutenthemera dziko lapansi, ndi maziko a mapiri ananjenjemera nagwedezeka, pakuti anakwiya Iyeyo.


Ndipo asaligulitse dziko chigulitsire; popeza dzikoli ndi langa; pakuti inu ndinu alendo akugonera ndi Ine.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa