Masalimo 40:1 - Buku Lopatulika1 Kuyembekeza ndayembekeza Yehova; ndipo anandilola, namva kufuula kwanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Kuyembekeza ndayembekeza Yehova; ndipo anandilola, namva kufuula kwanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Ine ndidayembekeza Chauta ndi mtima wokhulupirira kuti adzandithandize. Adaŵeramira pansi kuyang'ana kwa ine, namva kulira kwanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mofatsa ndinadikira Yehova Iye anatembenukira kwa ine ndipo anamva kulira kwanga. Onani mutuwo |