Masalimo 38:9 - Buku Lopatulika9 Ambuye, chikhumbo changa chonse chili pamaso panu; ndipo kubuula kwanga sikubisika kwa Inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ambuye, chikhumbo changa chonse chili pamaso panu; ndipo kubuula kwanga sikubisika kwa Inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ambuye, mumadziŵa zonse zimene ndimakhumba, kusisima kwanga sikuli kosamveka kwa Inu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Zokhumba zanga zonse zili poonekera pamaso panu Ambuye, kusisima kwanga sikunabisike kwa Inu. Onani mutuwo |