Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 38:8 - Buku Lopatulika

8 Ndafooka ine, ndipo ndachinjizidwa, ndabangula chifukwa cha kumyuka mtima wanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndafooka ine, ndipo ndachinjizidwa, ndabangula chifukwa cha kumyuka mtima wanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Ndatheratu, ndipo ndatswanyika. Ndikubuula chifukwa cha kuvutika mu mtima.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Ndilibe mphamvu ndipo ndakunthidwa kwathunthu; ndikubuwula ndi ululu wa mumtima.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 38:8
6 Mawu Ofanana  

Pakuti ndikati ndidye, kumadza kuusa moyo kwanga; ndi kudzuma kwanga kumathiridwa ngati madzi.


M'kati mwanga mupweteka mosapuma, masiku a mazunzo andidzera.


Ndiyenda ndili wothimbirira osati ndi dzuwa ai; ndinyamuka mumsonkhano ndi kufuula.


Pamene ndinakhala chete mafupa anga anakalamba ndi kubuula kwanga tsiku lonse.


Tonse tibangula ngati zilombo, ndi kulira maliro zolimba ngati nkhunda; tiyang'anira chiweruziro koma palibe; tiyang'anira chipulumutso koma chili patali ndi ife.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa