Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 38:7 - Buku Lopatulika

7 Pakuti m'chuuno mwanga mutentha kwambiri; palibe pamoyo m'mnofu mwanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Pakuti m'chuuno mwanga mutentha kwambiri; palibe pamoyo m'mnofu mwanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Thupi langa likutentha kwambiri ndi malungo, ndipo lilibe nyonga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Msana wanga wagwidwa ndi ululu wosasimbika, mulibe thanzi mʼthupi langa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 38:7
7 Mawu Ofanana  

Ndipo ndinati kwa mfumu, Mfumu ikhale ndi moyo kosatha; ilekerenji nkhope yanga kuchita chisoni, popeza pali bwinja kumzinda kuli manda a makolo anga, ndi zipata zake zopsereza ndi moto.


Mwa mphamvu yaikulu ya nthenda yanga chovala changa chinasandulika, chindithina ngati pakhosi pa malaya anga.


Mnofu wanga wavala mphutsi ndi nkanambo zadothi; khungu langa lang'ambika, nilinyansa.


Popeza masiku anga akanganuka ngati utsi, ndi mafupa anga anyeka ngati nkhuni.


Chamgwera chinthu choopsa, ati; popeza ali gonire sadzaukanso.


Ndipo pomwepo mngelo wa Ambuye anamkantha, chifukwa sanampatse Mulungu ulemerero; ndipo anadyedwa ndi mphutsi, natsirizika.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa