Masalimo 38:6 - Buku Lopatulika6 Ndapindika, ndawerama kwakukulu; ndimayenda woliralira tsiku lonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndapindika, ndawerama kwakukulu; ndimayenda woliralira tsiku lonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ndapindika msana kwathunthu, ndaŵerama zedi, ndatha mphamvu, tsiku lonse ndimangonka ndilira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ine ndapindika msana ndipo ndawerama kwambiri; tsiku lonse ndimangolira. Onani mutuwo |