Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 38:5 - Buku Lopatulika

5 Mabala anga anunkha, adaola, chifukwa cha kupusa kwanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Mabala anga anunkha, adaola, chifukwa cha kupusa kwanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Mabala anga aola ndipo akununkha chifukwa cha kupusa kwanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Mabala anga akuwola ndipo akununkha chifukwa cha uchitsiru wa moyo wanga wauchimo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 38:5
8 Mawu Ofanana  

ndipo ndinati, Mulungu wanga, ndigwa nkhope, ndi kuchita manyazi kuweramutsa nkhope yanga kwa inu Mulungu wanga, popeza mphulupulu zathu zachuluka pamutu pathu, ndi kupalamula kwathu kwakula kufikira mu Mwamba.


Pamene ndinakhala chete mafupa anga anakalamba ndi kubuula kwanga tsiku lonse.


Pakuti m'chuuno mwanga mutentha kwambiri; palibe pamoyo m'mnofu mwanga.


Ndikupemphani, Yehova, ndilanditseni; fulumirani kudzandithandiza, Yehova.


Wodala munthuyo mumsankha, ndi kumyandikizitsa, akhale m'mabwalo anu. Tidzakhuta nazo zokoma za m'nyumba yanu, za m'malo oyera a Kachisi wanu.


Mulungu, mudziwa kupusa kwanga; ndipo kutsutsika kwanga sikubisikira Inu.


Kodi mulibe vunguti mu Giliyadi? Kodi mulibe sing'anga m'menemo; analekeranji kuchira mwana wamkazi wa anthu anga?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa