Masalimo 38:10 - Buku Lopatulika10 Mtima wanga ugundagunda, mphamvu yanga yachoka, ndipo kuunika kwa maso anga, ndi iko komwe kwandichokera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Mtima wanga ugundagunda, mphamvu yanga yachoka, ndipo kuunika kwa maso anga, ndi iko komwe kwandichokera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Mtima wanga ukugunda, mphamvu zandithera, ndipo sindikutha kupenya bwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mtima wanga ukugunda, mphamvu zanga zikutha; ngakhale kuwala kwachoka mʼmaso mwanga. Onani mutuwo |