Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 38:3 - Buku Lopatulika

3 Mumnofu mwanga mulibe chamoyo chifukwa cha ukali wanu; ndipo m'mafupa anga simuzizira, chifukwa cha cholakwa changa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Mumnofu mwanga mulibe chamoyo chifukwa cha ukali wanu; ndipo m'mafupa anga simuzizira, chifukwa cha cholakwa changa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Thupi langa lilibe mphamvu chifukwa cha ukali wanu. M'nkhongono mwanga mwalobodoka chifukwa cha uchimo wanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Chifukwa cha ukali wanu mulibe thanzi mʼthupi langa; mafupa anga alibe mphamvu chifukwa cha tchimo langa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 38:3
13 Mawu Ofanana  

Koma Uziya anapsa mtima, mbale ya zofukiza ili m'dzanja lake kufukiza nayo; ndipo pakupsa mtima nao ansembe, khate linabuka pamphumi pake, pamaso pa ansembe m'nyumba ya Yehova, pambali pa guwa lofukizapo.


Pakuti mivi ya Wamphamvuyonse yandilowa, mzimu wanga uwumwa ulembe wake; zoopsa za Mulungu zindindandira nkhondo.


Popeza masiku anga akanganuka ngati utsi, ndi mafupa anga anyeka ngati nkhuni.


Chifukwa cha liu la kubuula kwanga mnofu wanga umamatika kumafupa anga.


Chifukwa usana ndi usiku dzanja lanu linandilemera ine; uwisi wanga unasandulika kuuma kwa malimwe.


Mundimvetse chimwemwe ndi kusekera, kuti mafupawo munawathyola akondwere.


Mundichitire chifundo, Yehova; pakuti ndalefuka ine. Mundichize, Yehova; pakuti anthunthumira mafupa anga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa