Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 38:21 - Buku Lopatulika

21 Musanditaye, Yehova, Mulungu wanga, musakhale kutali ndi ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Musanditaye, Yehova, Mulungu wanga, musakhale kutali ndi ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Musandisiye ndekha, Inu Chauta, Inu Mulungu wanga, musakhale nane kutali.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Inu Yehova, musanditaye; musakhale kutali ndi ine Mulungu wanga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 38:21
6 Mawu Ofanana  

Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine? Mukhaliranji kutali kwa chipulumutso changa, ndi kwa mau a kubuula kwanga?


Musandikhalire kutali; pakuti nsautso ili pafupi, pakuti palibe mthandizi.


Koma Inu, Yehova, musakhale kutali; mphamvu yanga Inu, mufulumire kundithandiza.


Pakuti sanapeputse ndipo sananyansidwe ndi zunzo la wozunzika; ndipo sanambisire nkhope yake; koma pomfuulira Iye, anamva.


Andibwezera choipa m'malo mwa chokoma, inde, asaukitsa moyo wanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa