Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 38:18 - Buku Lopatulika

18 Pakuti ndidzafotokozera mphulupulu yanga; nditenga nkhawa chifukwa cha tchimo langa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Pakuti ndidzafotokozera mphulupulu yanga; nditenga nkhawa chifukwa cha tchimo langa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Ndikuvomera kuipa kwanga, ndikuda nkhaŵa chifukwa cha machimo anga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Ndikuvomereza mphulupulu zanga; ndipo ndavutika ndi tchimo langa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 38:18
6 Mawu Ofanana  

Ngati ndakwirira zolakwa zanga monga Adamu, ndi kubisa mphulupulu yanga m'chifuwa mwanga;


Apenyerera anthu, ndi kuti, ndinachimwa, ndaipsa choongokacho, ndipo sindinapindule nako.


Ndinavomera choipa changa kwa Inu; ndipo mphulupulu yanga sindinaibise. Ndinati, Ndidzaululira Yehova machimo anga; ndipo munakhululukira choipa cha kulakwa kwanga.


Chifukwa ndazindikira machimo anga; ndipo choipa changa chili pamaso panga chikhalire.


Wobisa machimo ake sadzaona mwai; koma wakuwavomereza, nawasiya adzachitidwa chifundo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa