Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 38:17 - Buku Lopatulika

17 Ndafikana potsimphina, ndipo chisoni changa chili pamaso panga chikhalire.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndafikana potsimphina, ndipo chisoni changa chili pamaso panga chikhalire.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Inde, ndili pafupi kugwa, ndipo ndikumva kuŵaŵa nthaŵi zonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Pakuti ndili pafupi kugwa, ndipo ndikumva kuwawa nthawi zonse.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 38:17
8 Mawu Ofanana  

Koma ine ndakhulupirira pa chifundo chanu; mtima wanga udzakondwera nacho chipulumutso chanu.


Ndipo pakutsimphina ine anakondwera, nasonkhana pamodzi; akundipanda anandisonkhanira; ndipo sindinachidziwe, ananding'amba osaleka.


Adani anga asandikondwerere ine monyenga; okwiya nane kopanda chifukwa asanditsinzinire.


Ndapindika, ndawerama kwakukulu; ndimayenda woliralira tsiku lonse.


Ndalema nako kuusa moyo kwanga; ndiyandamitsa kama wanga usiku wonse; mphasa yanga ndiolobza ndi misozi yanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa