Masalimo 38:16 - Buku Lopatulika16 Pakuti ndinati, Asakondwerere ine; pakuterereka phazi langa, asadzikuze pa ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Pakuti ndinati, Asakondwerere ine; pakuterereka phazi langa, asadzikuze pa ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Popeza ndimapemphera kuti, “Musalole konse kuti akondwerere pa ine, amene amandinyodola akaona kuti ndikuterereka.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Pakuti Ine ndinati, “Musawalole kuti akondwere kapena kudzikweza okha pa ine pamene phazi langa laterereka.” Onani mutuwo |