Masalimo 38:15 - Buku Lopatulika15 Pakuti ndikuyembekezani Inu, Yehova; Inu mudzayankha, Ambuye Mulungu wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Pakuti ndikuyembekezani Inu, Yehova; Inu mudzayankha, Ambuye Mulungu wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Koma tsono ndimayembekezera Inu Chauta, Ndinu Chauta, Mulungu wanga amene mudzayankha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Ndikudikira Inu Yehova; mudzayankha, Inu Ambuye Mulungu wanga. Onani mutuwo |