Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 38:13 - Buku Lopatulika

13 Koma ine, monga gonthi, sindimva; ndipo monga munthu wosalankhula, sinditsegula pakamwa panga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Koma ine, monga gonthi, sindimva; ndipo monga munthu wosalankhula, sinditsegula pakamwa panga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Koma ine ndili ngati gonthi, sindikumvako, ndili ngati mbeŵeŵe amene satha kulankhula.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Ine ndili ngati munthu wosamva amene sangamve, monga wosayankhula, amene sangathe kutsekula pakamwa pake;

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 38:13
6 Mawu Ofanana  

Oipa ananditchera msampha; koma sindinasokere m'malangizo anu.


Ndinatonthola osanena mau, ndinakhala chete osalawa chokoma; ndipo chisoni changa chinabuka.


Ndinakhala duu, sindinatsegule pakamwa panga; chifukwa inu mudachichita.


Iye anatsenderezedwa koma anadzichepetsa yekha osatsegula pakamwa pake; ngati nkhosa yotsogoleredwa kukaphedwa, ndi ngati mwanawankhosa amene ali duu pamaso pa omsenga, motero sanatsegule pakamwa pake.


amene pochitidwa chipongwe sanabwezere chipongwe, pakumva zowawa, sanaopse, koma anapereka mlandu kwa Iye woweruza kolungama;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa