Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 38:14 - Buku Lopatulika

14 Inde ndikunga munthu wosamva, ndipo m'kamwa mwanga mulibe makani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Inde ndikunga munthu wosamva, ndipo m'kamwa mwanga mulibe makani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Inde ndili ngati munthu amene saamva, chifukwa sindingathe kuyankhapo kanthu, pamene akundilankhula.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Ndakhala ngati munthu amene samva, amene pakamwa pake sipangathe kuyankha.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 38:14
5 Mawu Ofanana  

Iye anatsenderezedwa koma anadzichepetsa yekha osatsegula pakamwa pake; ngati nkhosa yotsogoleredwa kukaphedwa, ndi ngati mwanawankhosa amene ali duu pamaso pa omsenga, motero sanatsegule pakamwa pake.


Chifukwa chake wochenjerayo akhala chete nthawi yomweyo; pakuti ndiyo nthawi yoipa.


Musakhulupirira bwenzi, musatama bwenzi loyanja; usamtsegulire pakhomo pakamwa pako, ngakhale kwa iye wogona m'fukato mwako.


Koma ichi ananena kuti amuyese Iye, kuti akhale nacho chomneneza Iye. Koma Yesu, m'mene adawerama pansi analemba pansi ndi chala chake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa