Masalimo 37:2 - Buku Lopatulika2 Pakuti adzawamweta msanga monga udzu, ndipo adzafota monga msipu wauwisi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pakuti adzawamweta msanga monga udzu, ndipo adzafota monga msipu wauwisi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 pakuti mosachedwa amanyala ngati udzu, ndipo amafota ngati masamba aaŵisi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 pakuti monga udzu iwo adzafota msanga, ngati mbewu zobiriwira adzanyala msanga. Onani mutuwo |