Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 37:1 - Buku Lopatulika

1 Usavutike mtima chifukwa cha ochita zoipa, usachite nsanje chifukwa cha ochita chosalungama.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Usavutike mtima chifukwa cha ochita zoipa, usachite nsanje chifukwa cha ochita chosalungama.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Usamavutika ndi anthu oipa. Usamakhumbira kukhala ngati ochita zoipa,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Usamavutike chifukwa cha anthu oyipa kapena kuchitira nsanje amene akuchita cholakwa;

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 37:1
12 Mawu Ofanana  

Anthu oongoka mtima adzadabwa nacho, ndi munthu wosalakwa adzadziutsa kumtsutsa wonyoza Mulunguyo.


Khala chete mwa Yehova, numlindirire Iye; usavutike mtima chifukwa cha iye wolemerera m'njira yake, chifukwa cha munthu wakuchita chiwembu.


Pakuti ndinachitira nsanje odzitamandira, pakuona mtendere wa oipa.


Utsiru wa munthu ukhotetsa njira yake; mtima wake udandaula pa Yehova.


Mtima wako usachitire nsanje akuchimwawo; koma opabe Yehova tsiku lonse.


Usachitire nsanje anthu oipa, ngakhale kufuna kukhala nao;


Usavutike mtima chifukwa cha ochita zoipa; ngakhale kuchitira nsanje amphulupulu.


Usachitire nsanje munthu wachiwawa; usasankhe njira yake iliyonse.


koma woipa sadzapeza bwino ngakhale kutanimphitsa masiku ake ngati mthunzi; chifukwa saopa pamaso pa Mulungu.


njiru, kuledzera, mchezo, ndi zina zotere; zimene ndikuchenjezani nazo, monga ndachita, kuti iwo akuchitachita zotere sadzalowa Ufumu wa Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa