Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 36:12 - Buku Lopatulika

12 Pomwepo padagwera ochita zopanda pake. Anawalikha, ndipo sadzatha kuukanso.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Pomwepo padagwera ochita zopanda pake. Anawalikha, ndipo sadzatha kuukanso.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Onani, ochita zoipa ali ngundangunda. Inu mwaŵagwetsa pansi ndipo sangathe kudzuka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Onani momwe ochita zoyipa agonera atagwa, aponyeni pansi, kuti asathe kudzukanso!

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 36:12
12 Mawu Ofanana  

Chifukwa chake oipa sadzaimirira pa mlanduwo, kapena ochimwa mu msonkhano wa olungama.


Makala amoto awagwere; aponyedwe kumoto; m'maenje ozama, kuti asaukenso.


Ndidzawapyoza kuti sangakhoze kuuka, adzagwa pansi pa mapazi anga.


Koma Inu, Mulungu, mudzawatsitsira kudzenje la chionongeko. Anthu okhetsa mwazi ndi achinyengo masiku ao sadzafikira nusu; koma ine ndidzakhulupirira Inu.


Anadziwika Yehova, anachita kuweruza, woipayo anakodwa ndi ntchito ya manja ake.


nuti, Chomwecho adzamira Babiloni, sadzaukanso chifukwa cha choipa chimene ndidzamtengera iye; ndipo adzatopa. Mau a Yeremiya ndi omwewo.


Ndani adzakhala wosaopa ndi wosalemekeza dzina lanu Ambuye? Chifukwa Inu nokha muli woyera; chifukwa mitundu yonse idzadza nidzalambira pamaso panu, popeza zolungama zanu zidaonetsedwa.


Adani anu onse, Yehova, atayike momwemo. Koma iwo akukonda Inu akhale ngati dzuwa lotuluka mu mphamvu yake. Ndipo dziko linapumula zaka makumi anai.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa