Masalimo 34:9 - Buku Lopatulika9 Opani Yehova, inu oyera mtima ake; chifukwa iwo akumuopa Iye sasowa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Opani Yehova, inu oyera mtima ake; chifukwa iwo akumuopa Iye sasowa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Muzimvera Chauta, inu anthu ake oyera mtima, pakuti amene amamumvera sasoŵa kanthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Wopani Yehova inu oyera mtima ake, pakuti iwo amene amaopa Iye sasowa kanthu. Onani mutuwo |