Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 34:10 - Buku Lopatulika

10 Misona ya mkango isowa nimva njala, koma iwo akufuna Yehova sadzasowa kanthu kabwino.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Misona ya mkango isowa nimva njala, koma iwo akufuna Yehova sadzasowa kanthu kabwino.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Ngakhale anaamkango amasoŵa chakudya ndipo amakhala anjala, koma anthu amene amalakalaka Chauta, sasoŵa zinthu zabwino.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Mikango itha kulefuka ndi kumva njala koma iwo amene amafunafuna Yehova sasowa kanthu kalikonse kabwino.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 34:10
11 Mawu Ofanana  

Misona ya mkango ibangula potsata nyama yao, nifuna chakudya chao kwa Mulungu.


M'nyumba mwake mudzakhala akatundu ndi chuma: Ndi chilungamo chake chikhala chikhalire.


Yehova ndiye mbusa wanga; sindidzasowa.


Kupulumutsa moyo wao kwa imfa, ndi kuwasunga ndi moyo m'nyengo ya njala.


Pakuti Yehova Mulungu ndiye dzuwa ndi chikopa; Yehova adzapatsa chifundo ndi ulemerero; sadzakaniza chokoma iwo akuyenda angwiro.


Yehova samvetsa njala moyo wa wolungama; koma amainga chifuniro cha wochimwa.


Kuopa Yehova kupatsa moyo; wokhala nako adzakhala wokhuta; zoipa sizidzamgwera.


Mphotho ya chifatso ndi kuopa Yehova ndiye chuma, ndi ulemu, ndi moyo.


Pakuti anthu akunja azifunitsa zonse zimenezo; pakuti Atate wanu wa Kumwamba adziwa kuti musowa zonse zimenezo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa