Masalimo 34:8 - Buku Lopatulika8 Talawani, ndipo onani kuti Yehova ndiye wabwino; wodala munthuyo wakukhulupirira Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Talawani, ndipo onani kuti Yehova ndiye wabwino; wodala munthuyo wakukhulupirira Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Yesani ndipo mudzaona kuti Chauta ndi wabwino. Ngwodala munthu wothaŵira kwa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Lawani ndipo onani kuti Yehova ndi wabwino; wodala munthu amene amathawira kwa Iye. Onani mutuwo |