Masalimo 34:4 - Buku Lopatulika4 Ndinafuna Yehova ndipo anandivomera, nandilanditsa m'mantha anga onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndinafuna Yehova ndipo anandivomera, nandilanditsa m'mantha anga onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ndidapemphera kwa Chauta ndipo adandiyankha. Adandipulumutsa kwa zonse zimene ndinkaziwopa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ine ndinafunafuna Yehova ndipo Iye anandiyankha; anandilanditsa ku mantha anga onse. Onani mutuwo |