Masalimo 34:2 - Buku Lopatulika2 Moyo wanga udzatamanda Yehova; ofatsa adzakumva nadzakondwera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Moyo wanga udzatamanda Yehova; ofatsa adzakumva nadzakondwera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Moyo wanga umanyadira Chauta. Anthu ozunzika amve ndipo akondwere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Moyo wanga udzanyadira Yehova; anthu osautsidwa amve ndi kukondwera. Onani mutuwo |