Masalimo 34:1 - Buku Lopatulika1 Ndidzalemekeza Yehova nyengo zonse; kumlemekeza kwake kudzakhala m'kamwa mwanga kosalekeza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndidzalemekeza Yehova nyengo zonse; kumlemekeza kwake kudzakhala m'kamwa mwanga kosalekeza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Ndidzayamika Chauta nthaŵi zonse, pakamwa panga padzatamanda Iye kosalekeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ndidzayamika Yehova nthawi zonse; matamando ake adzakhala pa milomo yanga nthawi zonse. Onani mutuwo |