Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 33:22 - Buku Lopatulika

22 Yehova, chifundo chanu chikhale pa ife, monga takuyembekezani Inu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Yehova, chifundo chanu chikhale pa ife, monga takuyembekezani Inu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Inu Chauta, chikondi chanu chosasinthika chikhale pa ife, chifukwa timakhulupirira Inu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Chikondi chanu chosatha chikhale pa ife Inu Yehova, pamene tikuyembekeza kwa Inu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 33:22
7 Mawu Ofanana  

Kumbukirani mau a kwa mtumiki wanu, amene munandiyembekezetsa nao.


Chifundo chanu chikhaletu chakunditonthoza, ndikupemphani, monga mwa mau anu kwa mtumiki wanu.


Koma ine ndakhulupirira pa chifundo chanu; mtima wanga udzakondwera nacho chipulumutso chanu.


Zisoni zambiri zigwera woipa; koma chifundo chidzamzinga iye wakukhulupirira Yehova.


Inu Yehova, mutikomere ife mtima; ife talindira Inu; mukhale dzanja lathu m'mawa ndi m'mawa, chipulumutso chathunso m'nthawi ya mavuto.


Pomwepo anakhudza maso ao, nati, Chichitidwe kwa inu monga chikhulupiriro chanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa