Masalimo 33:9 - Buku Lopatulika9 Pakuti ananena, ndipo chinachitidwa; analamulira, ndipo chinakhazikika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pakuti ananena, ndipo chinachitidwa; analamulira, ndipo chinakhazikika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 pakuti Iye adalankhula, ndipo zidachitikadi, adalamula, ndipo zidaonekadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pakuti Iye anayankhula ndipo zinakhalapo; Iye analamulira ndipo zinakhazikika. Onani mutuwo |