Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 33:8 - Buku Lopatulika

8 Dziko lonse lapansi liope Yehova, ponse pali anthu achite mantha chifukwa cha Iye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Dziko lonse lapansi liope Yehova, ponse pali anthu achite mantha chifukwa cha Iye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Dziko lonse lapansi liwope Chauta. Anthu onse okhala pa dziko lapansi achite naye mantha,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Dziko lonse lapansi liope Yehova; anthu onse amulemekeze Iye.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 33:8
10 Mawu Ofanana  

M'mwemo anthu amuopa, Iye sasamalira aliyense wanzeru mumtima.


Malekezero onse a dziko lapansi adzakumbukira nadzatembenukira kwa Yehova, ndipo mafuko onse a amitundu adzagwadira pamaso panu.


Mulungu adzatidalitsa; ndipo malekezero onse a dziko lapansi adzamuopa Iye.


Inu ndinu woopsa; ndipo utauka mkwiyo wanu adzakhala chilili ndani pamaso panu?


Pakuti Mulungu wathu ndiye moto wonyeketsa.


Ndani adzakhala wosaopa ndi wosalemekeza dzina lanu Ambuye? Chifukwa Inu nokha muli woyera; chifukwa mitundu yonse idzadza nidzalambira pamaso panu, popeza zolungama zanu zidaonetsedwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa