Masalimo 30:9 - Buku Lopatulika9 M'mwazi mwanga muli phindu lanji, potsikira ine kudzenje? Ngati fumbi lidzayamika Inu? Ngati lidzalalikira choonadi chanu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 M'mwazi mwanga muli phindu lanji, potsikira ine kudzenje? Ngati fumbi lidzayamika Inu? Ngati lidzalalikira choonadi chanu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 “Kodi mudzapindulanji pa imfa yanga ngati nditsikira ku manda? Kodi ine nditasanduka fumbi, ndingathe kukutamandani? Kodi pamenepo ndingathe kulalika za kukhulupirika kwanu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Kodi pali phindu lanji powonongeka kwanga ngati nditsikira ku dzenje? Kodi fumbi lidzakutamandani Inu? Kodi lidzalengeza za kukhulupirika kwanu? Onani mutuwo |