Masalimo 30:10 - Buku Lopatulika10 Mverani, Yehova, ndipo ndichitireni chifundo, Yehova, mundithandize ndi Inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Mverani, Yehova, ndipo ndichitireni chifundo, Yehova, mundithandize ndi Inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 “Imvani, Inu Chauta, ndipo mundikomere mtima. Inu Chauta, mukhale mthandizi wanga.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Imvani Yehova ndipo mundichitire chifundo; Yehova mukhale thandizo langa.” Onani mutuwo |