Masalimo 30:8 - Buku Lopatulika8 Ndinafuulira kwa Inu, Yehova; kwa Ambuye ndinapemba, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndinafuulira kwa Inu, Yehova; kwa Yehova ndinapemba, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Pamenepo ndidalirira Inu Chauta, ndipo ndidapempha chifundo chanu kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Kwa Inu Yehova ndinayitana; kwa Ambuye ndinapempha chifundo; Onani mutuwo |