Masalimo 30:4 - Buku Lopatulika4 Imbirani Yehova, inu okondedwa ake, ndipo yamikani pokumbukira chiyero chake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Imbirani Yehova, inu okondedwa ake, ndipo yamikani pokumbukira chiyero chake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Imbani nyimbo zotamanda Chauta, inu anthu ake oyera mtima, mumthokoze chifukwa cha dzina lake loyera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Imbirani Yehova inu anthu ake okhulupirika; tamandani dzina lake loyera. Onani mutuwo |