Masalimo 30:3 - Buku Lopatulika3 Yehova munabweza moyo wanga kumanda, munandisunga ndi moyo, kuti ndingatsikire kudzenje. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Yehova munabweza moyo wanga kumanda, munandisunga ndi moyo, kuti ndingatsikire kudzenje. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Inu Chauta, mwanditulutsa m'dziko la akufa, mwandibwezeranso moyo kuti ndingatsikire ku manda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Inu Yehova, munanditulutsa ku manda, munandisunga kuti ndisatsalire mʼdzenje. Onani mutuwo |