Masalimo 29:9 - Buku Lopatulika9 Liu la Yehova liswetsa nyama zazikazi, ndipo lipulula nkhalango; ndipo mu Kachisi mwake zonse zili m'mwemo zimati, Ulemerero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Liu la Yehova liswetsa nyama zazikazi, ndipo lipulula nkhalango; ndipo m'Kachisi mwake zonse zili m'mwemo zimati, Ulemerero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Liwu la Chauta likuzunguza miŵanga likupulula masamba a mitengo yonse m'dondo. Onse a m'nyumba mwake akufuula kuti, “Ulemererowo!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Liwu la Yehova limapindapinda mibawa ndi kuyeretsa nkhalango. Ndipo mʼNyumba mwake onse amafuwula kuti, “Ulemerero!” Onani mutuwo |