Masalimo 29:1 - Buku Lopatulika1 Perekani kwa Yehova, inu ana a amphamvu, perekani kwa Yehova ulemerero ndi mphamvu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Perekani kwa Yehova, inu ana a amphamvu, perekani kwa Yehova ulemerero ndi mphamvu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tamandani Chauta, inu okhala kumwamba. Tamandani ulemerero wake ndi mphamvu zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Perekani kwa Yehova, inu anthu amphamvu, perekani kwa Yehova ulemerero ndi mphamvu. Onani mutuwo |