Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 27:11 - Buku Lopatulika

11 Mundiphunzitse njira yanu, Yehova, munditsogolere panjira yachidikha, chifukwa cha adani anga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Mundiphunzitse njira yanu, Yehova, munditsogolere pa njira yachidikha, chifukwa cha adani anga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Mundiwonetse njira zanu zachifundo, Inu Chauta, munditsogolere m'njira yosalala, chifukwa ndili ndi adani ambiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Phunzitseni njira yanu Inu Yehova, munditsogolere mʼnjira yowongoka chifukwa cha ondizunza.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 27:11
22 Mawu Ofanana  

Ndinakufunani ndi mtima wanga wonse; ndisasokere kusiyana nao malamulo anu.


Ndipo mupenye ngati ndili nao mayendedwe oipa, nimunditsogolere panjira yosatha.


Munthuyo wakuopa Yehova ndani? Adzamlangiza iye njira adzasankheyo.


Adzawatsogolera ofatsa m'chiweruzo; ndipo adzaphunzitsa ofatsa njira yake.


Phazi langa liponda pachidikha, m'misonkhano ndidzalemekeza Yehova.


Yehova, munditsogolere m'chilungamo chanu, chifukwa cha akundizondawo; mulungamitse njira yanu pamaso panga.


Pakuti m'kamwa mwao mulibe mau okhazikika; m'kati mwao m'mosakaza; m'mero mwao ndi manda apululu; lilime lao asyasyalika nalo.


Adzabwezera choipa adani anga, aduleni m'choonadi chanu.


Afunafuna zosalungama; kusanthula, asanthuladi mpaka kutha; chingakhale cha m'kati mwake mwa munthu, ndi mtima wozama.


Mundionetse njira yanu, Yehova; ndidzayenda m'choonadi chanu, muumbe mtima wanga ukhale umodzi kuti uliope dzina lanu.


Mayendedwe a waulesi akunga linga laminga, koma njira ya oongoka mtima iundidwa ngati mseu.


Onsewo amveka ndi iye amene azindikira; alungama kwa akupeza nzeru.


Ndipo kudzakhala khwalala kumeneko, ndi njira, ndipo idzatchedwa njira yopatulika; odetsedwa sadzapita m'menemo; koma Iye adzakhala nao oyenda m'njira, ngakhale opusa, sadzasochera m'menemo.


Pakuti ndamva kugogodera kwa ambiri, mantha pozungulira ponse. Neneza, ndipo tidzamneneza iye, ati atsamwali anga onse, amene ayang'anira kutsimphina kwanga; kapena adzakopedwa, ndipo ife tidzampambana iye, ndipo tidzambwezera chilango.


Ndipo anamyang'anira, natumiza ozonda, amene anadzionetsera ngati olungama mtima, kuti akamkole pa mau ake, kotero kuti akampereke Iye ku ukulu ndi ulamuliro wa kazembe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa