Masalimo 27:10 - Buku Lopatulika10 Pakuti wandisiya atate wanga ndi amai wanga, koma Yehova anditola. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Pakuti wandisiya atate wanga ndi amai wanga, koma Yehova anditola. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ngakhale bambo wanga ndi mai wanga andisiye ndekha, Inu Chauta mudzandisamala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ngakhale abambo ndi amayi anga anditaya Yehova adzandisamala. Onani mutuwo |