Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 26:12 - Buku Lopatulika

12 Phazi langa liponda pachidikha, m'misonkhano ndidzalemekeza Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Phazi langa liponda pachidikha, m'masonkhano ndidzalemekeza Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Ndili wokhazikika pa malo opanda zovuta, ndipo ndidzatamanda Chauta pa msonkhano waukulu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Ndayima pa malo wopanda zovuta ndipo ndidzatamanda Yehova mu msonkhano waukulu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 26:12
11 Mawu Ofanana  

Amkwezenso mu msonkhano wa anthu, namlemekeze pokhala akulu.


Aleluya. Ndidzayamika Yehova ndi mtima wonse, mu upo wa oongoka mtima, ndi mumsonkhano.


Kumene akwerako mafuko, ndiwo mafuko a Yehova; akhale mboni ya kwa Israele, Ayamike dzina la Yehova.


kuti ndimveketse mau a chiyamiko, ndi kulalikira ntchito zanu zonse zozizwa.


Mundiphunzitse njira yanu, Yehova, munditsogolere panjira yachidikha, chifukwa cha adani anga.


Ndipo anandikweza kunditulutsa m'dzenje la chitayiko, ndi m'thope la pachithaphwi; nandipondetsa pathanthwe, nakhazika mayendedwe anga.


Apo pali Benjamini wamng'ono, wakuwachita ufumu, akulu a Yuda, ndi a upo wao, akulu a Zebuloni, akulu a Nafutali.


Woyenda moongoka amayenda osatekeseka; koma wokhotetsa njira zake adzadziwika.


Ndi kuti, Ndidzalalikira dzina lanu kwa abale anga, pakati pa Mpingo ndidzakuimbirani.


Adzasunga mapazi a okondedwa ake, koma oipawo adzawakhalitsa chete mumdima; pakuti palibe munthu adzapambana ndi mphamvu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa