Masalimo 25:3 - Buku Lopatulika3 Inde, onse akuyembekezera Inu sadzachita manyazi; adzachita manyazi iwo amene achita monyenga kopanda chifukwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Inde, onse akuyembekezera Inu sadzachita manyazi; adzachita manyazi iwo amene achita monyenga kopanda chifukwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Zoonadi, onse okhulupirira Inu asaŵachititse manyazi, koma muchititse manyazi onse ochita dala zosakhulupirika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Aliyense amene amayembekezera kwa Ambuye sadzachititsidwa manyazi koma achinyengo ndiwo adzachititsidwe manyazi ndipo sadzakhala ndi chodzitetezera. Onani mutuwo |