Masalimo 22:7 - Buku Lopatulika7 Onse akundipenya andiseka; akwenzula, apukusa mutu, nati, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Onse akundipenya andiseka; akwenzula, apukusa mutu, nati, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Onse ondiwona amandiseka, amandikwenzulira ndi kupukusa mitu yao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Onse amene amandiona amandiseka; amandiyankhulira mawu achipongwe akupukusa mitu yawo kunena kuti Onani mutuwo |