Masalimo 22:4 - Buku Lopatulika4 Makolo athu anakhulupirira Inu; anakhulupirira, ndipo munawalanditsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Makolo athu anakhulupirira Inu; anakhulupirira, ndipo munawalanditsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Makolo athu ankadalira Inu. Zoonadi, ankakhulupirira Inu, ndipo Inu munkaŵapulumutsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Pa inu makolo athu anadalira; iwo anadalira ndipo Inu munawapulumutsa. Onani mutuwo |
Ndipo kunali, pakuchita limodzi amalipenga ndi oimba, kumveketsa mau amodzi akulemekeza ndi kuyamika Yehova, ndi pakukweza mau ao pamodzi ndi malipenga, ndi nsanje, ndi zoimbira zina, ndi kulemekeza Yehova, ndi kuti, Pakuti Iye ndiye wabwino, pakuti chifundo chake chikhala chikhalire; pamenepo mtambo unadzaza nyumbayi, ndiyo nyumba ya Yehova;