Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 22:3 - Buku Lopatulika

3 Koma Inu ndinu woyera, wakukhala m'malemekezo a Israele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Koma Inu ndinu woyera, wakukhala m'malemekezo a Israele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Komabe Inu ndinu oyera, mumakhala pa mpando wanu waufumu, ndipo anthu anu Aisraele amakutamandani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Inu ndinu Woyera, wokhala pa mpando waufumu; ndinu matamando a Israeli.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 22:3
11 Mawu Ofanana  

Taonani, ndifuula kuti, Chiwawa! Koma sandimvera; ndikuwa, koma palibe chiweruzo.


Ndifuula kwa Inu, koma simundiyankha; ndinyamuka, ndipo mungondipenyerera.


Yehova ali wolungama m'njira zake zonse, ndi wachifundo m'ntchito zake zonse.


Wopereka nsembe yachiyamiko andilemekeza Ine; ndipo kwa iye wosunga mayendedwe ake ndidzamuonetsa chipulumutso cha Mulungu.


Mu Ziyoni akulemekezani Inu mwachete, Mulungu, adzakuchitirani Inu chowindachi.


Pemphero langa lidze pamaso panu; munditcherere khutu kukuwa kwanga.


Mkwezeni Yehova Mulungu wathu, ndipo gwadirani paphiri lake loyera; pakuti Yehova Mulungu wathu ndiye woyera.


Ndipo wina anafuula kwa mnzake, nati, Woyera, Woyera, Woyera, Yehova wa makamu; dziko lonse lapansi ladzala ulemerero wake.


Yehova, ndidzafuula mpaka liti osamva Inu? Ndifuulira kwa Inu za chiwawa, koma simupulumutsa.


Iye ndiye lemekezo lanu, Iye ndiye Mulungu wanu, amene anachita nanu zazikulu ndi zoopsa izi, mudaziona m'maso mwanu.


Ndipo zamoyozo zinai, chonse pa chokha chinali nao mapiko asanu ndi limodzi; ndipo zinadzala ndi maso pozinga ponse ndi m'katimo; ndipo sizipumula usana ndi usiku, ndi kunena, Woyera, woyera, woyera, Ambuye Mulungu Wamphamvuyonse, amene anali, amene ali, ndi amene alinkudza.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa