Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 22:2 - Buku Lopatulika

2 Mulungu wanga, ndiitana usana, koma simuvomereza; ndipo usiku, sindikhala chete.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Mulungu wanga, ndiitana usana, koma simuvomereza; ndipo usiku, sindikhala chete.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Mulungu wanga, ine ndimalira usana, koma Inu simundiyankha, ndimalira usiku, koma sindipeza mpumulo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Inu Mulungu wanga, ine ndimalira masana, koma simuyankha, usikunso, ndipo sindikhala chete.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 22:2
12 Mawu Ofanana  

Misozi yanga yakhala ngati chakudya changa, usana ndi usiku; pakunena iwo kwa ine dzuwa lonse, Mulungu wako ali kuti?


Yehova, Mulungu wa makamu, mudzakwiyira pemphero la anthu anu kufikira liti?


Yehova, Mulungu wa chipulumutso changa, ndinafuula pamaso panu usana ndi usiku.


Mwadzikuta ndi mtambo kuti pemphero lathu lisapyolemo.


Inde, pofuula ine ndi kuitana andithandize amakaniza pemphero langa.


Ndipo anawasiyanso, napemphera kachitatu, nateronso mau omwewo.


Ndipo kodi Mulungu sadzachitira chilungamo osankhidwa ake akumuitana usana ndi usiku, popeza aleza nao mtima?


Ndipo kunali masiku awa, Iye anatuluka nanka kuphiri kukapemphera; nachezera usiku wonse m'kupemphera kwa Mulungu.


ndi kuchulukitsa mapemphero athu usiku ndi usana kuti tikaone nkhope yanu, ndi kukwaniritsa zoperewera pa chikhulupiriro chanu?


Ndiyamika Mulungu, amene ndimtumikira kuyambira makolo anga ndi chikumbumtima choyera, kuti ndikumbukira iwe kosalekeza m'mapemphero anga,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa