Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 22:30 - Buku Lopatulika

30 Mbumba ya anthu idzamtumikira; kudzanenedwa za Ambuye ku mibadwo yakudza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Mbumba ya anthu idzamtumikira; kudzanenedwa za Ambuye ku mibadwo yakudza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Zidzukulu zam'tsogolo zidzatumikira Ambuye. Anthu adzauza mbadwo umene ukudzawo za Iye.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Zidzukulu zamʼtsogolo zidzamutumikira Iye; mibado ya mʼtsogolo idzawuzidwa za Ambuye.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 22:30
10 Mawu Ofanana  

Ana a atumiki anu adzakhalitsa, ndi mbeu zao zidzakhazikika pamaso panu.


Pamenepa anaopaopatu, pakuti Mulungu ali mu mbadwo wa wolungama.


Uwu ndi mbadwo wa iwo akufuna Iye, iwo akufuna nkhope yanu, Mulungu wa Yakobo.


ndikadati, Ndidzafotokozera chotere, taonani, ndikadachita chosakhulupirika ndi mbadwo wa ana ako.


Yehova adzawerenga, polembera mitundu ya anthu, uyu anabadwa komweko.


Koma kunakomera Yehova kumtundudza; anammvetsa zowawa; moyo wake ukapereka nsembe yopalamula, Iye adzaona mbeu yake, adzatanimphitsa masiku ake; ndipo chomkondweretsa Yehova chidzakula m'manja mwake.


ndipo musamayesa kunena mwa inu nokha, Atate wathu tili naye Abrahamu; pakuti ndinena kwa inu kuti mwa miyala iyi Mulungu akhoza kuukitsira Abrahamu ana.


Ndiponso, Ndidzamtama Iye. Ndiponso, Taonani, Ine ndi ana amene Mulungu anandipatsa.


Koma inu ndinu mbadwa yosankhika, ansembe achifumu, mtundu woyera mtima, anthu a mwini wake, kotero kuti mukalalikire zoposazo za Iye amene anakuitanani mutuluke mumdima, mulowe kuunika kwake kodabwitsa;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa