Masalimo 22:25 - Buku Lopatulika25 Lemekezo langa lidzakhala la Inu mu msonkhano waukulu, zowinda zanga ndidzazichita pamaso pa iwo akumuopa Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Lemekezo langa lidzakhala la Inu mu msonkhano waukulu, zowinda zanga ndidzazichita pamaso pa iwo akumuopa Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Ndidzakutamandani pa msonkhano waukulu chifukwa cha zimene mwandichitira. Zimene ndidalonjeza ndidzazichita pamaso pa onse okumverani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Ndidzakutamandani pa msonkhano waukulu chifukwa cha zimene mwandichitira. Ndidzakwaniritsa lonjezo langa pamaso pa amene amaopa Inu. Onani mutuwo |