Masalimo 21:6 - Buku Lopatulika6 Pakuti mumuikira madalitso kunthawi zonse; mumkondweretsa ndi chimwemwe pankhope panu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Pakuti mumuikira madalitso kunthawi zonse; mumkondweretsa ndi chimwemwe pankhope panu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Zoonadi, mwaisandutsa yodala kopambana mpaka muyaya. Mwaisangalatsa ndi chimwemwe, chifukwa muli nayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Zoonadi Inu mwayipatsa madalitso amuyaya, Inu mwayipatsa chisangalalo ndi chimwemwe chimene chili pamaso panu. Onani mutuwo |