Masalimo 21:2 - Buku Lopatulika2 Mwampatsa iye chikhumbo cha mtima wake, ndipo simunakane pempho la milomo yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Mwampatsa iye chikhumbo cha mtima wake, ndipo simunakana pempho la milomo yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mwaipatsa zimene mtima wake umakhumba, simudaimane zimene pakamwa pake padapempha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Inu mwayipatsa zokhumba za mtima wake ndipo simunayimane zopempha za pa milomo yake. Sela Onani mutuwo |