Masalimo 20:9 - Buku Lopatulika9 Yehova, pulumutsani, mfumuyo ativomereze tsiku lakuitana ife. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Yehova, pulumutsani, mfumuyo ativomereze tsiku lakuitana ife. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Inu Chauta, thandizani mfumu kuti ipambane. Mutiyankhe pamene tikuitana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Inu Yehova, pulumutsani mfumu! Tiyankheni pamene tikuyitanani! Onani mutuwo |