Masalimo 20:4 - Buku Lopatulika4 likupatse cha mtima wako, ndipo likwaniritse upo wako wonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 likupatse cha mtima wako, ndipo likwaniritse upo wako wonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Akupatse zimene mtima wako ukukhumba, akuthandize kuti zonse zimene wakonza zichitikedi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Akupatse chokhumba cha mtima wako ndipo akuthandize kuti zonse wakonza zichitike. Onani mutuwo |
Chifukwa chake mbuye wanga mfumu amvere mau a kapolo wake. Ngati ndi Yehova anakuutsirani inu kutsutsana ndi ine, alandire chopereka; koma ngati ndi ana a anthu, atembereredwe pamaso pa Yehova, pakuti anandipirikitsa lero kuti ndisalandireko cholowa cha Yehova, ndi kuti, Muka, utumikire milungu ina.